nya-x-nyanja_2ch_text_reg/25/07.txt

1 line
337 B
Plaintext

\v 7 Koma mwamuna wa Mulungu anabwela kuli eve nakukamba, "Mfumu, usavomeleze bankondo ba Israeli kuyenda naiwe, Yehova sali pakati pa Israeli- palibe muntu wa Efraimu. \v 8 Olo uyenda na kulimba mtima naku kosa kunkondo, Mulungu akuponya pansi pamenso pa mdani wako, pakuti Mulungu ndiye mphamvu yakutandiza, na mphamvu yakugwesa pansi.