nya-x-nyanja_2ch_text_reg/25/03.txt

1 line
411 B
Plaintext

\v 3 China bwela monga mwamusanga kulamulila kwake kunali kosilizaka bwino, anapaya bantchito bamene banapaya batatebake, mfumu. \v 4 Koma sanafake bana babo ku infa, monga mwamene vinalembewa mubuku ya Mose, monga Yehova analamulila, "bazi tate babo sibafunika kupaiwa chifukwa cha bana babo, na bana sibafunikila kupaiwa chifukwa chazi tate babo. koma, muntu aliyense afunikila kufa chifukwa cha chimo yake."