nya-x-nyanja_2ch_text_reg/24/20.txt

1 line
541 B
Plaintext

\v 20 Mzimu wa Mulungu unavalika Zekariya mwana wa wansembe Yehoyada. Zekariya anaimilila pamwamba pa bantu nat kukamba kuli beve, "Mulungu akamba ichi: Nchifukwa cha chani mupwanya malamulo ya Yehova, kuti musapambane? Popeza mwasiya Yehova, naeve akusiyani." \v 21 Koma anapangana; mfumu inalamulila, ana mutema miyala pa lubanza ya nyumba ya Yehova. \v 22 Yoasi mfumu inaibala, ba take Zekariya vamene bana muchitila. Mumalo mwake, anapaya mwana wa Yehoyada. pamene Zekariya anali pafupi nakufa, anakamba, "Yehova aone ichi na kukuitana."