nya-x-nyanja_2ch_text_reg/24/11.txt

1 line
574 B
Plaintext

\v 11 Vinachitika kuti ngati paliponse bokosi yaletewa kuli bakalonga ba mfumu na kwanja ya Alevi, ndipo paliponse ba kona kuti munali ndalama zambili, mlembi wa mfumu na wantchito wa mkulu wa wansembe angabwele, kuchosa bokosi, na kuitenga na kubweza mu malo yake. Banachita ichi siku na tsiku, kusonkesa ndalama zambili. \v 12 Mfumu ndi Yehoyada anapeleka ndalama kuli eve wamene anali kugwila ntchito yotumikila munyumba ya Yehova. Ba muna aba bana ngenesa amisili bamiyala na bamisili ba mataba kuti akonze nyumba ya Yehova, ndiponso ogwila ntchito zachisulo na zamkuwa.