nya-x-nyanja_2ch_text_reg/24/06.txt

1 line
409 B
Plaintext

\v 6 Mwaicho mfumu inaitana Yehoyada mkulu wa nsembe na kukamba kuli eve, “Chifukwa chiani sunapempe Alevi kuti babwelese kuchokela ku Yuda na ku Yerusalemu musonko yamene Mose mtumiki wa Yehova na kukumana kwa ba Israeli banapeleka pa tenti ya chipangano? " \v 7 Mwaicho bana ba muna ba Ataliya, mukazi woipa uja, anali anaononga nyumba ya Mulungu na kupeleka Abaala yonse yopatulika ya munyumba ya Yehova.