nya-x-nyanja_2ch_text_reg/24/01.txt

1 line
320 B
Plaintext

\c 24 \v 1 Yoasi anali na zaka zisanu ndi zibili pongena ufumu wake; Iye analamulila zaka 40 mu Yerusalemu. Amai bake banali Zibiya wa ku Beeriseba. \v 2 Yoasi anachita vofunikila pamenso pa Yehova masiku yonse ya wansembe Yehoyada. \v 3 Yehoyada anamtengela bakazi babili, ndipo anankala tate wa bana ba muna naba kazi.