nya-x-nyanja_2ch_text_reg/23/20.txt

1 line
373 B
Plaintext

\v 20 Yehoyada anatenga bosogolela ma magulu ya bantu 100, bantu olemekezeka, babwanamkubwa wa bantu, na bantu bonse muziko. Anachosa mfumu munyumba ya Yehova; bantu banangena pa Chipata Chakumwamba kufikila kunyumba ya mfumu nakala pampando wachifumu wa ufum. \v 21 Ndipo bantu bonse ba muziko anakondwela, na munzi munahala zee. Koma Ataliya anali ba namupaya na lupanga.