nya-x-nyanja_2ch_text_reg/23/08.txt

1 line
454 B
Plaintext

\v 8 Balevi na Bayuda bonse banatumikila mu njila monse, monga mwamene wansembe Yehoyada analamulila. Aliyense anatenga mwamuna wake, wamene anali kubwela kugwila ntchito pa Sabata, na bamene banafunikila kusiya kugwila ntchito pa Sabata, chifukwa wansembe Yehoyada sanachosepo gawo iliyonse. \v 9 Pamene wansembe Yehoyada anabwelesa kuli asogoleli munkondo na zikopa zazinga bangono na nabakulu zamene zinali za Mfumu Davide zinali mu nyumba ya Mulungu.