nya-x-nyanja_2ch_text_reg/23/06.txt

1 line
367 B
Plaintext

\v 6 Musa vomeleze kuti aliyense angene munyumba ya Yehova, kuchoselako bansembe na Alevi bamene bamtumikila. Banga ngene chifukwa nibo zipeleka. Koma bantu bena bonse bafunikila kumvela malamulo ya Yahweh. \v 7 Alevi azungulukila mfumu paliponse, muntu aliyense atenga zida zake mumanja. Aliyense ongena munyumba apaiwe. Muzinkala na mfumu ikangena kapena ikachoka."