nya-x-nyanja_2ch_text_reg/16/13.txt

1 line
342 B
Plaintext
Raw Permalink Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 13 Choncho Asa anagona pamodzi ndi makolo ake, ndipo anamwalira mchaka cha 41 cha ufumu wake. \v 14 Iwo anamuika mmanda ake amene anadzikwirira mu Mzinda wa Davide. Anamugoneka pa chithatha chodzaza ndi fungo labwino ndi zonunkhira zosiyanasiyana zokonzedwa ndi odziwa kununkhira. Kenako anasonkha moto waukulu kwambiri pomulemekeza.