nya-x-nyanja_2ch_text_reg/16/09.txt

1 line
331 B
Plaintext
Raw Permalink Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 9 Pakuti maso a Yehova ayangana pa dziko lonse lapansi, kuti adzionetsere wamphamvu kwa iwo amene mtima wawo uli wangwiro ndi Iye. Koma mwachita zopusa pankhaniyi. Kuyambira tsopano udzachita nkhondo.” \v 10 Pamenepo Asa anakwiyira wamasomphenyayo, ndipo anamuika mndende, pakuti anamukwiyira kwambiri pa nkhani imeneyi.