nya-x-nyanja_2ch_text_reg/16/07.txt

1 line
320 B
Plaintext
Raw Permalink Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 7 Nthawi imeneyo Hanani wamasomphenya anapita kwa Asa mfumu ya Yuda, nati kwa iye, “Popeza wadalira mfumu ya Aramu, osadalira Yehova Mulungu wako. Mdzanja lanu, \v 8 Aakusi ndi Alibia sanali gulu lalikulu lankhondo, ndi magaleta ankhondo ndi apakavalo ambiri, koma popeza munadalira Yehova, iye anakupulumutsani.