nya-x-nyanja_2ch_text_reg/16/02.txt

1 line
346 B
Plaintext
Raw Permalink Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 2 Pamenepo Asa anatulutsa siliva ndi golide mzosungiramo za mnyumba ya Yehova, ndi za mnyumba ya mfumu, nazitumiza kwa Beni-hadadi mfumu ya Aramu, wakukhala ku Damasiko. Iye anati: \v 3 “Pakhale pangano pakati pa ine ndi iwe, monga linali pakati pa bambo anga ndi atate wako. Taonani, ndakutumizirani siliva ndi golide. ine ndekha."