nya-x-nyanja_2ch_text_reg/14/14.txt

1 line
313 B
Plaintext
Raw Permalink Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 14 Koma khamu lankhondolo linawononga midzi yonse yozungulira Gerari, pakuti kuopa Yehova kunagwera okhalamo. Ankhondo anafunkha midzi yonse, ndipo munali zofunkha zambiri mmenemo. \v 15 Ankhondowo anawononga mahema a oŵeta ngombe; Anatenga nkhosa zambirimbiri ndi ngamila, kenako anabwerera ku Yerusalemu.