nya-x-nyanja_2ch_text_reg/14/09.txt

1 line
430 B
Plaintext
Raw Permalink Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 9 Zera Mkusi anadza kwa iwo ndi khamu la asilikali miliyoni imodzi, ndi magareta mazana atatu; anafika ku Maresha. \v 10 Kenako Asa anatuluka kukakumana naye, ndipo anakonza mizere yankhondo mchigwa cha Zefata ku Maresha. \v 11 Asa anafuulira kwa Yehova Mulungu wake, nati, Yehova, palibe wina, koma Inu, wothandiza wopanda mphamvu polimbana ndi ambiri. tabwera kudzamenyana ndi unyinji uwu, Yehova, inu ndinu Mulungu wathu;