nya-x-nyanja_2ch_text_reg/14/07.txt

1 line
438 B
Plaintext

\v 7 Pakuti Asa anauza Yuda kuti: “Tiyeni timange mizinda iyi, timange mipanda yozungulira, ndi nsanja, zipata, mipiringidzo, dziko likadali lathu chifukwa tafunafuna Yehova Mulungu wathu. mbali zonse.” Choncho anamanga ndipo anapambana. \v 8 Asa anali ndi gulu lankhondo lonyamula zishango ndi mikondo; A fuko la Yuda anali ndi amuna 300,000, ndi a Benjamini amuna 280,000 onyamula zishango ndi mauta. Onsewa anali ankhondo amphamvu.