nya-x-nyanja_2ch_text_reg/14/01.txt

1 line
480 B
Plaintext
Raw Permalink Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\c 14 \v 1 Abiya anagona pamodzi ndi makolo ake, ndipo anamuika mmanda mu Mzinda wa Davide. Asa mwana wake analowa ufumu mʼmalo mwake. Mmasiku ake dziko linali labata zaka khumi. \v 2 Asa anachita zabwino ndi zoyenera pamaso pa Yehova Mulungu wake, \v 3 pakuti anachotsa maguwa ansembe achilendo ndi misanje. Anaphwanya zipilala zamiyala ndi kugwetsa mizati ya Asera. \v 4 Iye anauza Yuda kuti afunefune Yehova Mulungu wa makolo awo, ndi kutsatira chilamulo + ndi malamulo.