nya-x-nyanja_2ch_text_reg/13/16.txt

1 line
320 B
Plaintext
Raw Permalink Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 16 Ana a Isiraeli anathawa pamaso pa Yuda, ndipo Yehova anawapereka mmanja mwa Yuda. \v 17 Abiya ndi ankhondo ake anawapha ndi kupha kwakukulu; Amuna osankhidwa a Isiraeli 500,000 anafa. \v 18 Momwemo anagonjetsedwa ana a Israyeli pa nthawiyo; Ana a Yuda anapambana chifukwa anadalira Yehova Mulungu wa makolo awo.