nya-x-nyanja_2ch_text_reg/13/10.txt

1 line
450 B
Plaintext
Raw Permalink Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 10 Koma ife, Yehova ndiye Mulungu wathu, + ndipo sitinamusiye. Tili ndi ansembe, zidzukulu za Aroni, otumikira Yehova, ndi Alevi amene amagwira ntchito yawo. \v 11 Mmawa ndi madzulo onse amafukizira Yehova nsembe zopsereza ndi zofukiza zonunkhira bwino. Iwo amakonzanso mkate woonekera patebulo loyera. azisamaliranso choikapo nyale chagolide, ndi nyali zake, aziyaka madzulo onse. Timasunga malamulo a Yehova Mulungu wathu, koma inu mwamusiya.