nya-x-nyanja_2ch_text_reg/13/06.txt

1 line
281 B
Plaintext
Raw Permalink Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 6 Koma Yerobiamu mwana wa Nebati, mtumiki wa Solomo mwana wa Davide, anaukira mbuye wake. \v 7 Anthu opanda pake, anthu opanda pake, anasonkhana kwa iye. Iwo anabwera kudzamenyana ndi Rehobowamu mwana wa Solomo, Rehobowamu ali wamngono ndi wantha mtima, + moti anamugonjetsa.