nya-x-nyanja_2ch_text_reg/13/04.txt

1 line
293 B
Plaintext
Raw Permalink Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 4 Abiya anaima paphiri la Zemaraimu, mdera lamapiri la Efuraimu, nkunena kuti: “Tamverani inu Yerobiamu ndi Aisiraeli onse. pangano la mchere? \v 5 Kodi simudziwa kuti Yehova Mulungu wa Israyeli anapatsa Davide ndi zidzukulu zake ulamuliro pa Israyeli kosatha ndi pangano la mchere?