nya-x-nyanja_2ch_text_reg/13/01.txt

1 line
428 B
Plaintext
Raw Permalink Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\c 13 \v 1 Mchaka cha 18 cha Mfumu Yerobiamu, Abiya anayamba kulamulira Yuda. \v 2 Anakhala mfumu zaka zitatu ku Yerusalemu; dzina la amake ndiye Makaya, mwana wamkazi wa Uriyeli wa ku Gibeya. Panali nkhondo pakati pa Abiya ndi Yerobiamu. \v 3 Abiya anapita kunkhondo ndi gulu lankhondo lamphamvu ndi olimba mtima, amuna osankhidwa 400,000. Yerobiamu anamuika ndi asilikali 800,000 osankhidwa mwapadera, ndi ngwazi zamphamvu.