nya-x-nyanja_2ch_text_reg/12/13.txt

1 line
393 B
Plaintext

\v 13 Chotero Mfumu Rehobowamu inalimbitsa ufumu wake ku Yerusalemu, ndipo anayamba kulamulira. Rehobowamu anali ndi zaka 41 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 17 ku Yerusalemu, mzinda umene Yehova anausankha pa mafuko onse a Isiraeli kuti aikepo dzina lake. Dzina la amayi ake linali Naama Mamoni. \v 14 Iye anachita zoipa chifukwa sanakhazikitse mtima wake kufunafuna Yehova.