nya-x-nyanja_2ch_text_reg/12/09.txt

1 line
387 B
Plaintext
Raw Permalink Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 9 Choncho Sisaki mfumu ya Iguputo inabwera kudzamenyana ndi Yerusalemu nkutenga chuma cha mnyumba ya Yehova, ndi chuma cha mnyumba ya mfumu. Iye anachotsa chirichonse; anatenganso zishango zagolide zimene Solomo anapanga. \v 10 Mfumu Rehobowamu inapanga zishango zamkuwa mmalo mwake, nkuzipereka mmanja mwa akuluakulu a asilikali olondera zitseko za nyumba ya mfumu.