nya-x-nyanja_2ch_text_reg/12/05.txt

1 line
327 B
Plaintext
Raw Permalink Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 5 Tsopano mneneri Semaya anabwera kwa Rehobowamu ndi kwa atsogoleri a Yuda amene anasonkhana ku Yerusalemu chifukwa cha Sisaki. Semaya anati kwa iwo, Atero Yehova, Inu mwandisiya ine, chotero inenso ndakuperekani mdzanja la Sisaki. \v 6 Pamenepo akalonga a Israyeli ndi mfumu anadzichepetsa, nati, Yehova ndiye wolungama.