nya-x-nyanja_2ch_text_reg/10/15.txt

1 line
155 B
Plaintext

\v 15 Choncho mfumuyo sinamvere anthuwo, chifukwa Mulungu anasinthadi kuti Yehova akwaniritse mawu amene Ahiya wa ku Silo anauza Yerobiamu mwana wa Nebati.