nya-x-nyanja_2ch_text_reg/10/12.txt

1 line
384 B
Plaintext

\v 12 Choncho Yerobiamu ndi anthu onse anabwera kwa Rehobowamu tsiku lachitatu, monga mfumu inati, “Mubwere kwa ine tsiku lachitatu. \v 13 Mfumu Rehobowamu analankhula nawo mwaukali, osanyalanyaza malangizo a akuluwo. \v 14 Analankhula nao monga mwa uphungu wa anyamatawo, nati, Atate wanga anakulemeretsa goli lanu, koma ine ndidzaonjezerapo. Atate wanga anakukwapulani ndi zikoti;