nya-x-nyanja_2ch_text_reg/10/10.txt

1 line
372 B
Plaintext
Raw Permalink Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 10 Anyamata amene anakulira pamodzi ndi Rehobowamu anamuuza kuti: “Ukauze anthu amene anakuuzani kuti Solomo atate wanu analemetsa goli lawo, koma inu mulipeputse. ukawauze kuti, Chala changa chachingono nchachikulu kuposa chiuno cha atate wanga, \v 11 ndipo tsopano, ngakhale kuti bambo anga anakusenzetsani goli lolemera, ine ndidzakukwapulani ndi zikoti."