nya-x-nyanja_2ch_text_reg/10/01.txt

1 line
268 B
Plaintext

\c 10 \v 1 Rehobowamu anaenda ku Sekemu, pakuti Israyeli yonse inali kubwela ku Sekemu kumuika kunkala mfumu. \v 2 Pamene Yelobowamu mwana wa Nebati anamvela vamene ivi (chifukwa anali ku Igupto, kwamene anathabila kuyopa Mfumu Solomo), anabwelela kuchokela ku Igupto.