nya-x-nyanja_2ch_text_reg/09/29.txt

1 line
473 B
Plaintext

\v 29 Monga pa khani zinangu zokamba pali Solomoni, zoyamba na zosiliza, nanga sizinalembewe mu mbili ya muneneli Natani, mu uneneli wa Ahiya wa ku Silo, na mumasomphenya ya Iddo oona.(wamene naye anali na utenga pali Yeroboamu mwana mwamuna wa Nebat)? \v 30 Solomoi analamulila bonse ba Israeli mu Yerusalemu kwa zaka 40. \v 31 Anagona pamozi na makolo yake ndipo banamuyika mumanda mu muzinda wa Davide batate bake. Rehobowamu, mwana wake, anankala nfumu mumalo mwake.