nya-x-nyanja_2ch_text_reg/09/22.txt

1 line
371 B
Plaintext

\v 22 Momwemo Mfumu Solomoni inachila mafumu yonse ya maziko yapansi mu chuma ndi nzelu. \v 23 Mafumu yonse yapa ziko lapansi yamafuna pamenso pa Solomoni kuti banvele nzelu zake, zamene Mulungu anaziyika mumutima mwake. \v 24 Bamabwela kuzapeleka musonko, zibiya zasiliva ndi zagolide, zovala, zida zankhondo, ndi zonunkhiritsa, komanso akavalo na nyulu, chaka na chaka.