nya-x-nyanja_2ch_text_reg/09/17.txt

1 line
373 B
Plaintext

\v 17 Ndipo mfumu inapanga mupando wachifumu waukulu wa minyanga ya njovu ndipo unakuta na golide woyengeka bwino kwambili. \v 18 Mpando wachifumuwo unali na masitepe yasanu na limozi, ndipo chopondapo mapazi chinali cholumikizidwa pampandowo. Kumbali iliyonse ya mpandowo panali mipando yolumikizila mikono iwili na mikango ibili inaimilila pambali pa chilichonse cha izi.