nya-x-nyanja_2ch_text_reg/09/10.txt

1 line
552 B
Plaintext

\v 10 Banchito ba Hiramu na banchito ba Solomoni, amene anabweretsa golide kuchokera ku Ofiri, anabwelesa matabwa ya mlamu ndi myala ya mutengo wapatali. \v 11 Mfumu inakonza masitepe a nyumba ya Yehova, ndi nyumba yake, na zeze, na azeze ndi azeze za oimbila; Mitengo ngati yamene inalibe kuonekapo mu ziko ya Yuda. \v 12 Mfumu Solomoni inapeleka kwa mfumukazi ya ku Seba chilichonse chamene inkafuna na chilichonse chamene inapempa; anamupasa vambili kuchila vamene inabwelesa ku mfumu. Ndipo inachoka na kubwelela ku ziko yake, eve na banchito bake.