nya-x-nyanja_2ch_text_reg/09/01.txt

1 line
433 B
Plaintext

\c 9 \v 1 Pamene Mfumukazi yaku Seba inanvela utenga pali Solomoni, anabwela ku Yerusalemu kuti amuyese na mafunso yolimba. Anabwela na kalavani yayitali kwambili, na ngamila zozula na vonunkila, golide yambili, na myala yamutengo wapatali yambili. Pamene anafika kuli Solomoni, anamuuza vonse vamene vinali mumutima wake. \v 2 Solomoni anamuyanka yonse mafunso yake; kunalibe chovuta kuli Solomoni; kunalibe funso yamene sanayanke.