nya-x-nyanja_2ch_text_reg/07/13.txt

1 line
461 B
Plaintext

\v 13 Nanga ngati navala kumwamba kuti kulibe nvula, kapena nalamulila zombekuononga ziko, kapena nikatuma matenda pakati pa bantu banga, \v 14 ndipo ngati bantu banga, bamene baitaniwa pazina yanga, bazazichepesa, kupempela, nakufuna nkope yanga, na kuchoka kunjila zawo zoipa, nianvela kuchoka kumwamba, kubakululukila machimo yawo, na kupolesa ziko yawo. \v 15 Manje nizasegula menso yanga na makutu yanga kunvela ku mapempelo yamene yachitikila pamalo yano.