nya-x-nyanja_2ch_text_reg/07/11.txt

1 line
339 B
Plaintext

\v 11 Momwemo Solomoni anasiliza kumanga nyumba ya Yehova na nyumba yake. Chilichonse chamene chinabwela mumutima wa Solomoni kupanga mu nyumba ya Yehova na munyumba yake, anachikwanilisa bwino. \v 12 Yehova anaonekela kuli Solomoni usiku nakumuuza kuti, "Nanvela pempelo yako, ndipo nazisankila yano malo monga nyumba yopelekelamo nsembe.