nya-x-nyanja_2ch_text_reg/07/01.txt

1 line
539 B
Plaintext

\c 7 \v 1 Manje pamene Solomoni anasiliza kupempela, mulilo unabwela pansi kuchoka kumwmba na kushoka nsembe zoshoka na nsembe zopasa, ndipo ulemelelo wa Yehova unazula mu nyumba. \v 2 Bansembe sibanakwanise kungena mu nyumba ya Yehova, chifukwa ulemelelo wake unazula munyumba yake. \v 3 Pamene bana ba Israyeli banaona mulilo ubwela pansi na ulemelelo wa Yehova pamwamba pa nyumba, banagwada pansi nankope zawo pansi pa mwala woikika na kulambila na kuyamika Yehova. Banati, "Pakuti ni wabwino, chifukwa chipangano chake nichamuyayaya."