nya-x-nyanja_2ch_text_reg/02/11.txt

1 line
403 B
Plaintext

\v 11 Pamene apo Hiramu, mfumu ya ku Turo, anayanka na kulemba, nakutumiza kuli Solomo,'' nakukamba, pakuti Yehova akonda bantu bake, anakuyika iwe mfumu yao. \v 12 Kuwonjezerapo, Hiramu anakamba, "Adalisike Yehova, Mulungu wa Israeli, wamene analenga kumwamba na ziko yapansi, wamene anapasa mfumu Davide mwana wanzelu, wanzelu na woziba, bamene bazamangila Yehova nyumba na nyumba ya ufumu yake mwine.