From faa4d5976d9bfb51b7065e1b81a37253b5773953 Mon Sep 17 00:00:00 2001 From: Muzgatama Date: Thu, 18 Apr 2024 11:50:19 +0200 Subject: [PATCH] Thu Apr 18 2024 11:50:18 GMT+0200 (South Africa Standard Time) --- 14/14.txt | 2 +- 15/01.txt | 1 + 15/03.txt | 1 + 15/title.txt | 1 + manifest.json | 2 +- 5 files changed, 5 insertions(+), 2 deletions(-) create mode 100644 15/01.txt create mode 100644 15/03.txt create mode 100644 15/title.txt diff --git a/14/14.txt b/14/14.txt index 99d0c81..53d251a 100644 --- a/14/14.txt +++ b/14/14.txt @@ -1 +1 @@ -+ Koma khamu lankhondolo linawononga midzi yonse yozungulira Gerari, + pakuti kuopa + Yehova kunagwera okhalamo. Ankhondo anafunkha midzi yonse, ndipo munali zofunkha zambiri mmenemo. Ankhondowo anawononga mahema a oŵeta ng’ombe; + Anatenga nkhosa + zambirimbiri ndi ngamila, kenako anabwerera ku Yerusalemu. \ No newline at end of file +\v 14 Koma khamu lankhondolo linawononga midzi yonse yozungulira Gerari, pakuti kuopa Yehova kunagwera okhalamo. Ankhondo anafunkha midzi yonse, ndipo munali zofunkha zambiri mmenemo. \v 15 Ankhondowo anawononga mahema a oŵeta ng’ombe; Anatenga nkhosa zambirimbiri ndi ngamila, kenako anabwerera ku Yerusalemu. \ No newline at end of file diff --git a/15/01.txt b/15/01.txt new file mode 100644 index 0000000..2468780 --- /dev/null +++ b/15/01.txt @@ -0,0 +1 @@ +\c 15 \v 1 Mzimu wa Mulungu unadza pa Azariya mwana wa Odedi. \v 2 Anatuluka kukakumana ndi Asa n’kumuuza kuti: “Ndimvereni, Asa, ndi Ayuda onse ndi Benjamini: Yehova ali nanu pamene inu muli ndi iye. Musiyeni, adzakusiyani. \ No newline at end of file diff --git a/15/03.txt b/15/03.txt new file mode 100644 index 0000000..ae101bb --- /dev/null +++ b/15/03.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 3 \v 5 Tsopano kwa nthawi yaitali, Israyeli analibe Mulungu woona, wopanda wansembe wophunzitsa, ndiponso wopanda chilamulo. \v 4 Koma m’masautso awo anatembenukira kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi kumufunafuna, ndipo anamupeza. M’masiku amenewo munalibe mtendere kwa iye wotuluka kapena amene ankalowa, chifukwa panali chipwirikiti chachikulu pa anthu onse okhala m’dzikolo. \ No newline at end of file diff --git a/15/title.txt b/15/title.txt new file mode 100644 index 0000000..59d27b9 --- /dev/null +++ b/15/title.txt @@ -0,0 +1 @@ +Mutu 15 \ No newline at end of file diff --git a/manifest.json b/manifest.json index e6434f1..223e4ca 100644 --- a/manifest.json +++ b/manifest.json @@ -161,9 +161,9 @@ "14-07", "14-09", "14-12", + "14-14", "15-title", "15-01", - "15-03", "15-06", "15-08", "15-10",