Thu Dec 09 2021 14:59:59 GMT+0000 (Greenwich Mean Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-12-09 14:59:59 +00:00
parent 85a4ebf9d3
commit e0010f86a2
3 changed files with 3 additions and 3 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 15 Yehoyada anakula ndipo anali na zaka zambili, ndipo anafa; anali ndi zaka 130 atamwalira. \v 16 Anamuika m'manda mu Mzinda wa Davide pakati pa mafumu, chifukwa anachita zabwino mu Israeli, kwa Mulungu ndi ku nyumba ya Mulungu.
\v 15 Yehoyada anakula ndipo anali na zaka zambili, ndipo anafa; anali na zaka 130 pamene anafa. \v 16 Bana mushika mumanda mu Mzinda wa Davide pakati pa mafumu, chifukwa anachita zabwino mu Israeli, kwa Mulungu na ku nyumba ya Mulungu.

View File

@ -1 +1 @@
\v 17 Pambuyo pa imfa ya Yehoyada, atsogoleri a ku Yuda anabwera ndi kulemekeza mfumu. Kenako mfumuyo inawamvera. \v 18 Anasiya nyumba ya Yehova, Mulungu wa makolo ao, napembedza milungu yopatulika ndi mafano. Mkwiyo wa Mulungu unagwera Yuda ndi Yerusalemu chifukwa cha kulakwa kwawo. \v 19 Koma anatumiza aneneri kwa iwo kuti awabwezeretse kwa iye, Yehova; aneneri adachitira umboni anthu, koma iwo adakana kumvera.
\v 17 Pambuyo pa imfa ya Yehoyada, asogoleli a ku Yuda anabwera ndi kulemekeza mfumu. Kenako mfumuyo inawamvera. \v 18 Anasiya nyumba ya Yehova, Mulungu wa makolo ao, napembedza milungu yopatulika ndi mafano. Mkwiyo wa Mulungu unagwera Yuda ndi Yerusalemu chifukwa cha kulakwa kwawo. \v 19 Koma anatumiza aneneri kwa iwo kuti awabwezeretse kwa iye, Yehova; aneneri adachitira umboni anthu, koma iwo adakana kumvera.

View File

@ -284,7 +284,7 @@
"24-08",
"24-11",
"24-13",
"24-17",
"24-15",
"24-20",
"24-23",
"24-25",