Thu Apr 18 2024 10:50:07 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Timothy Muzgatama 2024-04-18 10:50:08 +02:00
parent 0688624c48
commit de2299a99d
2 changed files with 1 additions and 1 deletions

1
10/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 \v 4 \v 5 Mwamene umo banatumiza mau na kumuitana, ndipo Yelobowamu pamozi na Aisrayeli onse anadza; analankhula ndi Rehobowamu nati, "Atate wako anapangitsa goli lathu kukhala lovuta. Choncho, pangani khama la atate wako kukhala losavuta, ndi kupeputsa goli lolemera limene anativeka, ndipo tidzakutumikirani." Rehobowamu anawauza kuti, "Bweranso kwa ine patatha masiku atatu." Choncho anthuwo ananyamuka.

View File

@ -118,7 +118,6 @@
"09-29",
"10-title",
"10-01",
"10-03",
"10-06",
"10-08",
"10-10",