From c4d5a62eb74100995bbd855700dbc92470dc55c0 Mon Sep 17 00:00:00 2001 From: Muzgatama Date: Thu, 18 Apr 2024 11:08:11 +0200 Subject: [PATCH] Thu Apr 18 2024 11:08:11 GMT+0200 (South Africa Standard Time) --- 10/16.txt | 1 + 1 file changed, 1 insertion(+) create mode 100644 10/16.txt diff --git a/10/16.txt b/10/16.txt new file mode 100644 index 0000000..afa32ad --- /dev/null +++ b/10/16.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 16 Aisrayeli onse ataona kuti mfumu sinawamvere, anthu anamuyankha n’kunena kuti, "Kodi Davide ali ndi gawo lotani? Tilibe cholowa mwa mwana wa Jese! Aliyense wa inu abwerere ku hema wake, Israyeli. Tsopano onani kunyumba kwanu, David." Chotero Aisrayeli onse anabwerera ku mahema awo. \ No newline at end of file