diff --git a/10/16.txt b/10/16.txt new file mode 100644 index 0000000..afa32ad --- /dev/null +++ b/10/16.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 16 Aisrayeli onse ataona kuti mfumu sinawamvere, anthu anamuyankha n’kunena kuti, "Kodi Davide ali ndi gawo lotani? Tilibe cholowa mwa mwana wa Jese! Aliyense wa inu abwerere ku hema wake, Israyeli. Tsopano onani kunyumba kwanu, David." Chotero Aisrayeli onse anabwerera ku mahema awo. \ No newline at end of file