Thu Apr 18 2024 10:46:06 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Timothy Muzgatama 2024-04-18 10:46:07 +02:00
parent eecc19d061
commit c4b8197e75
1 changed files with 1 additions and 0 deletions

1
10/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 10 Rehobowamu anaenda ku Sekemu, pakuti Israyeli yonse inali kubwela ku Sekemu kumupanga kukhala mfumu. 2 Pamene Yerobiamu mwana wa Nebati anamva zimenezi (pakuti anali ku Igupto, kumene anathaŵa kwa Mfumu Solomo), anabwerera kuchokera ku Igupto.