Thu Apr 18 2024 10:25:10 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Timothy Muzgatama 2024-04-18 10:25:11 +02:00
commit c378f7e16c
121 changed files with 506 additions and 2 deletions

1
02/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 2 \v 1 Manje solomoni analamulila kuti bamange nyumba ya zina ya Yehova na kumananga nyumba ya ufumu mu ufumu wake. \v 2 Solomo anaika bamuna 70,000 bonyamula katundu, na bamuna 80,000 kuti bankale bojuba myala kumalupili, na bamuna 3,600 kuti bazibayanganila. \v 3 Pamene apo Solomo anatumiza mau kuli Hiramu mfumu ya ku Turo, kukamba kuti, “Monga mwamene munachitila na tate wanga Davide, pakumutumizila mitengo ya mkunguza kuti amange nyumba yonkalamo, imwe muchite so chabe na kuli ine.

1
02/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 Ona nasala pan'gono kumangila nyumba zina ya Yehova Mulungu wanga, kuti niyipatule, na kuputiza vonunkila pamenso pake, kupeleka mukate wopatulika, na nsembe zopseleza kuseni na kumazulo, pa Masabata na pa myezi yanyowani, na pa mapwando yo yikiwa ya Yehova Mulungu watu. ivi niva ntau zonse, kuli Israeli. \v 5 Nyumba yamene nizamanga izankala ikulu maningi, chifukwa mulungu watu ni mukulu kuchila milungu zinango zonse.

1
02/06.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 6 Koma nindani angakwanise kumangila Mulungu nyumba, pakuti cholengewa chonse ngankale kumwamba sikungankale na eve? Ndine ndani kuti nimumangile nyumba, koma kuperekela nsembe zopsereza pamenso pake? \v 7 ndiye Chifukwa chake nitumizileni muntu waluso pa nchito ya golide, siliva, mkuwa, chisulo, na nyula ya chibakuwa, yofiila, na tonje yamanzi; azankala na bamuna baluso bamene bali na ine ku Yuda na ku Yerusalemu, bamene Davide tate banga anapasa.

1
02/08.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 8 Nitumizileni futi mitengo ya mkunguza, mkunguza, na mialigamu yochokela ku Lebanoni, chifukwa niziba kuti batumiki banu bamaziba kujuba mitengo ku Lebanoni. onani, banyamata banga bazankala na bakapolo banu, \v 9 kuti banikonzele mitengo yambili; \v 10 onani, nizapasa bakapolo banu, bamene bazadula mitengo, zikwi makumi yabili ya tiligu, makilogilamu zikwi makumi yabili ya balele, malita makumi yabili ya vinyo, na misuko ya mafuta zikwi makumi yabili.

1
02/11.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 11 Pamene apo Hiramu, mfumu ya ku Turo, anayanka na kulemba, nakutumiza kuli Solomo,'' nakukamba, pakuti Yehova akonda bantu bake, anakuyika iwe mfumu yao. \v 12 Kuwonjezerapo, Hiramu anakamba, "Adalisike Yehova, Mulungu wa Israeli, wamene analenga kumwamba na ziko yapansi, wamene anapasa mfumu Davide mwana wanzelu, wanzelu na woziba, bamene bazamangila Yehova nyumba na nyumba ya ufumu yake mwine.

1
02/13.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 13 Manje natumiza muntu waluso, Huram-Abi, wamene anapasiwa mpaso yo mvesesa. \v 14 Na mwana mwamuna wa mukazi wa bana bakazi ba Dani. Batate bake banali ba ku turo. eve ni waluso pa nchito yagolide, siliva, yamkuwa, yachisulo, yamyala, yamitengo, na yofiirira, yamtambo, na yofiira, na bafuta yotelela. Futi niwaluso mukupanga vili vonse vo beza futi na kapangidwe ka vili vonse vosiyanasiyana. Mumupase malo pakati pa ba nchito banu baluso, na kuli ba Ambuye wanga Davide tate wanu.

1
02/15.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 15 Manje tiligu, balele, mafuta na vinyo, vamene mbuye wanga mwanena, atumize ivi kuli bakapolo bake. Tijuba mitengo kuchokela ku Lebanoni, mitengo yambili yamene munga fune. \v 16 Tizayenda na imwe monga matanga yoyenda panyanja kuyenda ku Yopa, ndipo imwe muyende nabo ku Yerusalemu. "

1
02/17.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 17 Ndipo Solomo anabelenga balendo bonse bonkala muziko ya Israyeli, monga machitidwe Anababelenga Davide, atate bake. Beve banapezeka kuti benze 153,600. \v 18 Anabapasa bantu 70,000 kuti banyamule katundu, benango 80,000 kuti bankale Bojuba myala mumapili, ndipo 3,600 bankale boyang'anila bantu bogwila nchito.

1
02/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 2

1
07/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 7 \v 1 Manje pamene Solomoni anasiliza kupempela, mulilo unabwela pansi kuchoka kumwmba na kushoka nsembe zoshoka na nsembe zopasa, ndipo ulemelelo wa Yehova unazula mu nyumba. \v 2 Bansembe sibanakwanise kungena mu nyumba ya Yehova, chifukwa ulemelelo wake unazula munyumba yake. \v 3 Pamene bana ba Israyeli banaonamulilo ubwela pansi na ulemelelo wa Yehova pamwamba pa nyumba, banagwada pansi nankope zawo pansi pa mwala woikika na kulambila na kuyamika Yehova. Banati, "Pakuti ni wabwino, chifukwa chipangano chake nichamuyayaya."

1
07/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 Ndipo mfumu na bantu bonse banapeleka nsembe kwa Yehova. \v 5 Mfumu Solomoni inapeleka nsembe ya ng'ombe 22,000 na nkosa na mbuzi 120,000. Ndipo mfumu na bantu bonse banaipeleka nyumba ya Mulungu. \v 6 Bansembe banaimilila, aliyense kuimilila kwamene asebenzela; ma Levi nawo navilimba vawo vanyimbo kwa Yehova, vamene Davide mfumu anapanga zoyamikila Yehova munyimbo, "Chifukwa chipangano chake chili chamuyayaya." Bonse bansembe banaliza malupenga pasogolo pawo, ndipo Israeli yonse inaimilila.

1
07/07.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 7 Solomoni anapatula pakati pa bwalo pasogolo pa nyumba ya Yehova. Kwamene uko anapeleka nsembe zoshoka na mafuta ya nsembe za kuyanjana, chifukwa guwa yansembe yamukuwa yamene banamanga siinakwanise kugwila nsembe zoshoka, nsembe zambeu na zamafuta.

1
07/08.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 8 Ndipo Solomoni anachita chikondwelelo masiku yali 7, na bonse ba Israeli, musonkano waukulu kwambili, kuchokela ku Lebo Hamati mpaka ku mumana wa ku Igupto. \v 9 Pa siku lachisanu na chitatu anachita musonkano waukulu, chifukwa anapatulila guwa ya bansembe masiku yasanu na yabili, na madyelelo masiku yasanu na yabili. \v 10 Pa siku ya 23 ya mwezi wachisanu na chibili, Solomoni anatuma bantu kuti bayende ku matenti yawo na chimwemwe na mitima yokondwela chifukwa cha zabwino zamene Yehova anachitila Davide, Solomoni, na Israeli, bantu bake.

1
07/11.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 11 Momwemo Solomoni anasiliza kumanga nyumba ya Yehova na nyumba yake. Chilichonse chamene chinabwela mumutima wa Solomoni kupanga mu nyumba ya Yehova na munyumba yake, anachikwanilisa bwino. \v 12 Yehova anaonekela kuli Solomoni usiku nakumuuza kuti, "Nanvela pempelo yako, ndipo nazisankila yano malo monga nyumba yopelekelamo nsembe.

1
07/13.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 13 Nanga ngati navala kumwamba kuti kulibe nvula, kapena nalamulila zombekuononga ziko, kapena nikatuma matenda pakati pa bantu banga, \v 14 ndipo ngati bantu banga, bamene baitaniwa pazina yanga, bazazichepesa, kupempela, nakufuna nkope yanga, na kuchoka kunjila zawo zoipa, nianvela kuchoka kumwamba, kubakululukila machimo yawo, na kupolesa ziko yawo. \v 15 Manje nizasegula menso yanga na makutu yanga kunvela ku mapempelo yamene yachitikila pamalo yano.

1
07/16.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 16 Chifukwa nasanka na kupatula ino nyumba kuti zina yanga izankalapo muyayaya. Menso yanga na mutima wanga yazankala kwamene uko masiku yonse. \v 17 Koma iwe, ukayenda pamenso panga monga Davide batate bako banayendela, kumvelela vonse vamene nakulamulila, na kusunga malamulo yanga, malemba anga, \v 18 nizankazikisa mupando wako wachifumu, monga ninakambila muchipangano na Davide batate bako , pamene ninakamba kuti, 'Mwana wako sazakangiwa kunkala olamulila Isiraeli.'

1
07/19.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 19 Koma ngati wachokako, na kukana malemba na malamulo yanga yamene naika pasogolo pako, ndipo ukayenda kupembeza milungu inangu na kuigwadila, \v 20 nizabachosa kuchoka mu ntaka yamene nabapasa. Iyi nyumba yamene naipatula chifukwa cha zina yanga, nizayitaya kuchoka pamenso panga, ndipo nizaipanga mwambo na chosekewa mukati mwa bantu.

1
07/21.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 21 Ngakhale iyi tempele niyokwela kwambili, aliyense wamene azapita pafupi azadabwa eka. Bazafunsa kuti, 'Nichifukwa chani Yehova achita izi ziko lino na nyumba iyi?' \v 22 Benangu bazayanka, 'Chifukwa banakana Yehova, Mulungu wawo, wamene anabwelesa makolo yawo kuchoka mu ziko ya Aiguputo, ndipo banagwililila milungu inangu ndi kuigwadira na kuigwadia na kuipembeza. Ndiye chifukwa chake Yehova abwelesa chionongeko ichi chonse."

1
08/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 8 \v 1 Chinachitika kuti pa kusila kwa zaka 20, pamene Solomoni anamanga nyumba ya Yehova na nyumba yake, \v 2 Solomoni anamanganso mizinda imene Hiramu anamupasa, nakunkazikamo bana ba Israeli.

1
08/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 Solomoni anaukila Hamati-Soba na kubagonjesa. \v 4 Anamanga Tadimori muchipululu, na yonse mizinda yosungilamo chuma, yamene anamanga ku Hamati.

1
08/05.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 5 Anamanganso Betihoroni Wakumwamba, na Betihoroni Wamunyashi, mizinda yochingiliwa na vipupa, komo, na mipilingizo. \v 6 Solomoni anamanga Balati na mizinda yonse yosungilamo vintu vamene anali navo, mizinda yonse ya magaleta yake, na mizinda ya bantu bokwela pamahachi yake, na chilichonse chamene anafuna kumanga ponvela bwino ku Yerusalemu, ku Lebanoni, na mumaziko yonse pansi pa ulamulilo wake.

1
08/07.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 7 Kwa bantu bonse bamene banasala baku Ahiti, Aamori, Aperezi, Ahivi, na Ayebusi, bamene sibanali baku Israeli, \v 8 Bazukulu bawo bamene banasala pambuyo pawo mu ziko, bamene bana ba Isiraeli sibanaononge - Solomoni anabangenesa munchito zokakamiza, zamene ziliko namanje.

1
08/09.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 9 Mwaichi, Solomoni sanapange bakapolo kuchoka ku Israeli. Mumalo mwake, banakhala basilikali bake, bakazembe bake, bakapitawo bake, na aakazembe ba magaleta yake, na bapakavalo yake. \v 10 Bamene abo banali woyanganila amene banali kuyanganila mfumu Solomoni, bali 250, bamene banali kuyanganila bantu bamene banali kugwila nchito.

1
08/11.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 11 Solomo anatenga mwana wamukazi wa Farao kuchokela ku Muzinda wa Davide kupita naye ku nyumba yamene anamumangila, chifukwa anati, "Mukazi wanga sayenela kunkala nyumba ya Davide mfumu ya Israeli, chifukwa kulikonse kwamene likasa ya Yehova yapita kunkala koyera. "

1
08/12.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 12 Ndipo Solomoni anapeleka nsembe zoshoka kwa Yehova paguwa yake yansembe yamene anamanga pasogolo pa konde. \v 13 Anapeleka nsembe monga mwa masiku na siku yobwela; anazipasa, kukonka malangizo yamene yapezeka mumalamulo ya Mose, pa masiku ya Sabata, mu mwezi wamanje, napantawi yoikika yamadyelelo katatu muchaka chilichonse: Madyelelo ya buledi ilibe chofufumusa, madyelelo yapa sabata, na madyelelo ya misasa.

1
08/14.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 14 Mukusunga malamulo ya Davide batate bake, Solomoni anasanka vigawo va bansembe pa nchito yawo, na Alevi pa nchito zawo, kuti balemekeze Mulungu na kutumikila pamenso pa bansembe, monga mwamene chifunikila kunkalila siku ndi siku. Anasanka futi olonda muvigawo pa komo iliyonse, ya Davide, muntu wa Mulungu, anavikambapo ivi. \v 15 Aba bantu sibanapatuke kuchoka ku malamulo ya mfumu kuyenda ku bansembe nama Levi vokuza nkani iliyonse, kapena yokuza vipinda vosungilamo.

1
08/16.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 16 Nchito zonse zamene Solomoni analamulila zinasila, kuchokela pamene maziko ya nyumba ya Yehova yanayafaka kufikila pamene inasila. Nyumba ya Mulungu inasila.

1
08/17.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 17 Pamenepo Solomoni anayenda ku Ezioni Geberi na kuyenda ku Elati ku gombe, ku ziko ya Edomu. \v 18 Hiramu anamutumizila boti yolamulila banchito bake, bamene banaziba nyanja, na banchito ba Solomoni banayenda ku Ofiri ndipo banatenga 450 matumba ya golide nakuyabwelesa kuli mfumu Solomoni.

1
09/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 9 \v 1 Pamene Mfumukazi yaku Seba inanvela utenga pali Solomoni, anabwela ku Yerusalemu kuti amuyese na mafunso yolimba. Anabwela na kalavani yayitali kwambili, na ngamila zozula na vonunkila, golide yambili, na myala yamutengo wapatali yambili. Pamene anafika kuli Solomoni, anamuuza vonse vamene vinali mumutima wake. \v 2 Solomoni anamuyanka yonse mafunso yake; kunalibe chovuta kuli Solomoni; kunalibe funso yamene sanayanke.

1
09/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 Pamene Mfumukazi yaku Seba inaona nzelu za Solomoni na nyumba yaufumu yamene anamanga, \v 4 vakudya pa tebulo yake, ponkala pa banchito bake, nchito za banchito bake na vovala vawo, omupelekela chiko na vovala vawo, na nsembe zoshoka zamene anapeleka ku nyumba ya Yehova, munalibe na mpepo muli eve.

1
09/05.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 5 Anakamba kuli mfumu, "Nizoona, utenga wamene ninanvela mu ziko mwanga pa mau yako na panzelu zako. \v 6 Sininakulupilile vamene ninanvela mpaka pamene ninabwela kuno, ndipo menso yanga yaviona. Sipakati ninauziwa paza ukulu wa nzelu na chuma chako! Wachilapo pa utenga wamene ninanvela.

1
09/07.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 7 Niwodalisika kwambili bamuna bako, ndipo niwodalisika banchito bako bamene baimilila pasogolo pako, chifukwa banvela nzelu zako. \v 8 Adalisike Yehova Mulungu wako, wamene amakondwela naiwe, wamene anakufaka pamupando wake, kunkala mfumu ya Yehova Mulungu wako. Chifukwa Mulungu wako anakonda Israyeli, kuti abankazikise ku ntawi zonse, ndipo anakuikani kunkala mfumu yao, kuti muchite chiweluzo na chilungamo.

1
09/09.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 9 Anapasa mfumu matalente 120 yagolide, na zonunkila zambili, na myala yamutengo wapatali. Palibe zonunkila bwino zambili kuchila izi kuchila zamene mfumukazi ya ku Seba inapasa Mfumu Solomo zinapasiwa kuli eve.

1
09/10.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 10 Banchito ba Hiramu na banchito ba Solomoni, amene anabweretsa golide kuchokera ku Ofiri, anabwelesa matabwa ya mlamu ndi myala ya mutengo wapatali. \v 11 Mfumu inakonza masitepe a nyumba ya Yehova, ndi nyumba yake, na zeze, na azeze ndi azeze za oimbila; Mitengo ngati yamene inalibe kuonekapo mu ziko ya Yuda. \v 12 Mfumu Solomoni inapeleka kwa mfumukazi ya ku Seba chilichonse chamene inkafuna na chilichonse chamene inapempa; anamupasa vambili kuchila vamene inabwelesa ku mfumu. Ndipo inachoka na kubwelela ku ziko yake, eve na banchito bake.

1
09/13.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 13 Manje kulema kwa golide yamene inali kubwela kwa Solomoni mu chaka chimozi inali matalente 666 yagolide, \v 14 kuwonjezela pa golide yamene bamalonda na amalonda banali kubwelesa. Mafumu yonse yaku Arabiya na babwana mukubwa mu ziko nawo banabwelesa golide na siliva kwa Solomoni.

1
09/15.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 15 Mfumu Solomoni anapanga vishango vikulu vili 200 va golide yopangika. Masekeli yali 600 ya golide yanangenelana. \v 16 Anapanganso vishango vili 300 va golide wopondelezedwa. Mainasi yatatu yagolide ya pachikopa chilichonse; mfumu inaziponya munyumba ya musanga ya Lebano.

1
09/17.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 17 Ndipo mfumu inapanga mupando wachifumu waukulu wa minyanga ya njovu ndipo unakuta na golide woyengeka bwino kwambili. \v 18 Mpando wachifumuwo unali na masitepe yasanu na limozi, ndipo chopondapo mapazi chinali cholumikizidwa pampandowo. Kumbali iliyonse ya mpandowo panali mipando yolumikizila mikono iwili na mikango ibili inaimilila pambali pa chilichonse cha izi.

1
09/19.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 19 Mikango khumi ndi zibili zinaimilila pamakwelelo, imozi kumbali kwa inzake ya wina mbali iyi na imozi ya masitepe yasanu na limozi. Panalibe mupando wachifumu wolingana nauyo mu ufumu wina uliwonse. \v 20 Chiko chili chonse chomwelamo Mfumu Solomoni chinali chagolide, na chiko chilichonse zakumwa mu Nyumba ya Nkhalango ya Lebanoni zinali za golide boyenga bwino. Kunalibe chinali cha chifukwa siliva sibanali kuipenda mu masiku ya Solomoni. \v 21 Mfumu inali na zombo zapanyanja zambili, pamozi na zombo za Hiramu. Kamozi lyonse pa zaka zitatu zombozi zimabwelesa golide, siliva, minyanga ya njovu, komanso anyani na anyani.

1
09/22.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 22 Momwemo Mfumu Solomoni inachila mafumu yonse ya maziko yapansi mu chuma ndi nzelu. \v 23 Mafumu yonse yapa ziko lapansi yamafuna pamenso pa Solomoni kuti banvele nzelu zake, zamene Mulungu anaziyika mumutima mwake. \v 24 Bamabwela kuzapeleka musonko, zibiya zasiliva ndi zagolide, zovala, zida zankhondo, ndi zonunkhiritsa, komanso akavalo na nyulu, chaka na chaka.

1
09/25.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 25 Solomoni anali na makola 4,000 ya mahachi na magaleta, na bapakavalo 12,000, bamene anayika mumizinda ya magaleta na ku Yerusalemu. \v 26 Anakalamulila mafumu yonse kuyambila ku Mumana mpaka ku ziko ya Afilisiti, mpaka kumalile na Igupto.

1
09/27.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 27 Mfumu inali na siliva mu Yerusalemu, monga chabe minyala ili pansi. Anapanganso matabwa a mukunguza yolingana na mitengo ya mukuyu yamene ili ku chigwa. \v 28 Banabwelesa mahachi ya Solomoni kuchokela ku Igupto na maziko yonse.

1
09/29.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 29 Monga pa khani zinangu zokamba pali Solomoni, zoyamba na zosiliza, nanga sizinalembewe mu mbili ya muneneli Natani, mu uneneli wa Ahiya wa ku Silo, na mumasomphenya ya Iddo oona.(wamene naye anali na utenga pali Yeroboamu mwana mwamuna wa Nebat)? \v 30 Solomoi analamulila bonse ba Israeli mu Yerusalemu kwa zaka 40. \v 31 Anagona pamozi na makolo yake ndipo banamuyika mumanda mu muzinda wa Davide batate bake. Rehobowamu, mwana wake, anankala nfumu mumalo mwake.

1
23/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 23 \v 1 Muchaka cha 7, Yehoida anaonesa mphamvu zake na kuchita chipangano naba sogoleli ba magulu ya bantu muma gulu 100, Azariya mwana wa Yerohamu, Ismayeli mwana wa Yehohanani, Azariya mwana wa Obedi, Maseya mwana wa Adaya, na Elisafati mwana wa Zikiri. \v 2 Banayendayenda mu Yuda na kusonkana Alevi kuchokela mumizinda zonse za Yuda, na basogoleli ba mabanja ya Israyeli, ndipo banabwela ku Yerusalemu. \v 3 Zonse msonkano zina panga pangano na mfumu munyumba ya Mulungu; Yehoyada anababuza kuti, “Onani, mwana wa mfumu azalamulila monga mwamene Yehova anakambila pali bana naba bazikulu ba Davide.

1
23/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 Ichi ndiye chamene mufunikila kuchita: Gawo imozi wa magawo yatatu ya basembe na Alevi bamene bamabwela kutumikila pa Sabata bazankala balonda pakomo. \v 5 Winangu wachitatu azankala kunyumba ya mfumu, ndipo winangu wachitatu azankala pachipata. Bantu bonse bazankala palubanza ya nyumba ya Yehova.

1
23/06.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 6 Musa vomeleze kuti aliyense angene munyumba ya Yehova, kuchoselako bansembe na Alevi bamene bamtumikila. Banga ngene chifukwa nibo zipeleka. Koma bantu bena bonse bafunikila kumvela malamulo ya Yahweh. \v 7 Alevi azungulukila mfumu paliponse, muntu aliyense atenga zida zake mumanja. Aliyense ongena munyumba apaiwe. Muzinkala na mfumu ikangena kapena ikachoka."

1
23/08.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 8 Balevi na Bayuda bonse banatumikila mu njila monse, monga mwamene wansembe Yehoyada analamulila. Aliyense anatenga mwamuna wake, wamene anali kubwela kugwila ntchito pa Sabata, na bamene banafunikila kusiya kugwila ntchito pa Sabata, chifukwa wansembe Yehoyada sanachosepo gawo iliyonse. \v 9 Pamene wansembe Yehoyada anabwelesa kuli asogoleli munkondo na zikopa zazinga bangono na nabakulu zamene zinali za Mfumu Davide zinali mu nyumba ya Mulungu.

1
23/10.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 10 Yehoyada anagwila bankondo bonse, aliyense anyamula chida chake mumanja, kuyambila mbali yakumanja ya Nyumba mpaka mbali ya kumanzele ku Nyumba, mubymbali mwa guwa yansembe koma nyumba yoyandikana nayo. \v 11 Ndipo banachosa mwana mwamuna wamfumu, nakumuvalika chisote chaufumu na kumupasa malamulo ya mapangano. Ndipo bana mupanga mfumu, ndipo Yehoyada na bana bake anamuzoza. ndipo bana kamba, "Mfumu inkale na moyo utali."

1
23/12.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 12 Ataliya ananvela chongo cha bantu kutamanga na kutamanda mfumu, anabwela kuli bantu mu nyumba ya Yehova., \v 13 ndipo anaona, mfumu inaimilila pambali pa chipilala chake pakomo, na bakazembe na kuimba malipenga yanali pafupi na mfumu. Bantu bonse mziko banali kusangalala ndipo banali kuimba malipenga, ndipo oyimba anali kuimba zida zoimbila na kusogolela kuimba nyimbo zotamanda Mulungu. Ataliya anangamba vovala vake na kupunda, "Chiwembu! Chiwembu!"

1
23/14.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 14 Ndipo wansembe Yehoyada anachosa bosogolela mazana akuyanganila nkondo, na kukamba kuli beve, ''Muchoseni pakati pa magulu; aliyense wamene azamukonka, lekani apaiwe na lupanga.'' Popeza wansembe anakamba, Usamupaile munyumba ya Yehova.' \v 15 Anamugwila pamene anali kungen pachipata cha matchi * cha munyumba ya mfumu, na ku mupaya.

1
23/16.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 16 Yehoyada anachita pangano pakati pa beve, bantu bonse na mfumu, kuti azankala bantu ba Yehova. \v 17 Mwaicho bantu bonse anayenda ku nyumba ya Baala, naigwesa. Anapwanya maguwa ya Baala na mafano yake, nda mupaya Matani, wansembe wa Baala pasogolo pa maguwa.

1
23/18.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 18 Yehoyada anaika oyanganila nyumba ya Yehova mosamalila wansembe, Alevi, wamene Davide anabapasa nyumba ya Yehova, kuti apeleke nsembe zopseleza kuli Yehova, monga mwalembewa mucilamulo cha Mose, ndi kusekelela na kuimba monga Davide analangiza. \v 19 Yehoyada anaika bolonda pazipata za nyumba ya Yehova kuti aliyense wadoti mu njila iliyonse asangene.

1
23/20.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 20 Yehoyada anatenga bosogolela ma magulu ya bantu 100, bantu olemekezeka, babwanamkubwa wa bantu, na bantu bonse muziko. Anachosa mfumu munyumba ya Yehova; bantu banangena pa Chipata Chakumwamba kufikila kunyumba ya mfumu nakala pampando wachifumu wa ufum. \v 21 Ndipo bantu bonse ba muziko anakondwela, na munzi munahala zee. Koma Ataliya anali ba namupaya na lupanga.

1
24/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 24 \v 1 Yoasi anali na zaka zisanu ndi zibili pongena ufumu wake; Iye analamulila zaka 40 mu Yerusalemu. Amai bake banali Zibiya wa ku Beeriseba. \v 2 Yoasi anachita vofunikila pamenso pa Yehova masiku yonse ya wansembe Yehoyada. \v 3 Yehoyada anamtengela bakazi babili, ndipo anankala tate wa bana ba muna naba kazi.

1
24/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 China bwela pasogolo pa ichi, kuti Yoasi anaganiza kumangamo nyumba ya Yehova. \v 5 Anasonkanisa bansembe na Alevi, ndipo anabauuza, "Yendani chaka chilichonse muzabwela pamozi ku mizinda wa Yuda Israeli yonse ndalama kusonkela nyumba ya Mulungu wanu. Onesani kuti muyamba ntawi yamene iyi." Alevi sanachite chilichonse poyamba.

1
24/06.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 6 Mwaicho mfumu inaitana Yehoyada mkulu wa nsembe na kukamba kuli eve, “Chifukwa chiani sunapempe Alevi kuti babwelese kuchokela ku Yuda na ku Yerusalemu musonko yamene Mose mtumiki wa Yehova na kukumana kwa ba Israeli banapeleka pa tenti ya chipangano? " \v 7 Mwaicho bana ba muna ba Ataliya, mukazi woipa uja, anali anaononga nyumba ya Mulungu na kupeleka Abaala yonse yopatulika ya munyumba ya Yehova.

1
24/08.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 8 Mwaicho mfumu inalamula, banatenga likasa, nakuika panja pakomo pa nyumba ya Yehova. \v 9 Mwaicho analengiza pakati pa Yuda na Yerusalemu, kuti bantu abelese kwa Yehova musonko wamene Mose mtumiki wa Mulungu aalipila Israeli muchipululu. \v 10 Asogoleli bonse na bantu bonse banakondwela na kubwelesa ndalama na kuziyika mubokosi mpaka bana siliza kufakamo.

1
24/11.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 11 Vinachitika kuti ngati paliponse bokosi yaletewa kuli bakalonga ba mfumu na kwanja ya Alevi, ndipo paliponse ba kona kuti munali ndalama zambili, mlembi wa mfumu na wantchito wa mkulu wa wansembe angabwele, kuchosa bokosi, na kuitenga na kubweza mu malo yake. Banachita ichi siku na tsiku, kusonkesa ndalama zambili. \v 12 Mfumu ndi Yehoyada anapeleka ndalama kuli eve wamene anali kugwila ntchito yotumikila munyumba ya Yehova. Ba muna aba bana ngenesa amisili bamiyala na bamisili ba mataba kuti akonze nyumba ya Yehova, ndiponso ogwila ntchito zachisulo na zamkuwa.

1
24/13.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 13 Mwaicho ba muna bogwila ntchito banagwia ntchito yo konza inayenda pasogolo mu manja mwabo; Banamanga nyumba ya Mulungu monga mwamene banapangila poyamba na kuilimbisa. \v 14 Pamene bana siliza, banabwelesa ndalama zinasalapo kuli mfumu na Yehoyada. Ndalama izi banasebenzesa ntchito popangila vibiya va muyumba ya Yehova, vibiya zogwilisilamo ntchito na popeleka zopeleka — makapu na zibiya zagolide na zasiliva. Banali kupeleka nsembe munyumba ya Yehova kupitiliza masiku yonse a Yehoyada.

1
24/15.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 15 Yehoyada anakula ndipo anali na zaka zambili, ndipo anafa; anali na zaka 130 pamene anafa. \v 16 Bana mushika mumanda mu Mzinda wa Davide pakati pa mafumu, chifukwa anachita zabwino mu Israeli, kwa Mulungu na ku nyumba ya Mulungu.

1
24/17.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 17 Pambuyo pa imfa ya Yehoyada, asogoleli ba kwa Yuda banabwela na kulemekeza mfumu. Mwaicho mfumu inabanvela. \v 18 Banasiya nyumba ya Yehova, Mulungu wa makolo yabo, na kumpembeza milungu yopatulika na mafano. Ukali wa Mulungu unagwela Yuda na Yerusalemu chifukwa cha kulakwa kwabo. \v 19 Koma anatumiza baneneli kuli beve kuti ababwezelese kuli eve, Yehova; baneneli anachitila umboni antu, koma banakana ku kumvela.

1
24/20.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 20 Mzimu wa Mulungu unavalika Zekariya mwana wa wansembe Yehoyada. Zekariya anaimilila pamwamba pa bantu nat kukamba kuli beve, "Mulungu akamba ichi: Nchifukwa cha chani mupwanya malamulo ya Yehova, kuti musapambane? Popeza mwasiya Yehova, naeve akusiyani." \v 21 Koma anapangana; mfumu inalamulila, ana mutema miyala pa lubanza ya nyumba ya Yehova. \v 22 Yoasi mfumu inaibala, ba take Zekariya vamene bana muchitila. Mumalo mwake, anapaya mwana wa Yehoyada. pamene Zekariya anali pafupi nakufa, anakamba, "Yehova aone ichi na kukuitana."

1
24/23.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 23 Kosilizila chaka, gulu yankondo inabwela kumenyana na Yowasi. Bana bwela kuli Yuda na ku Yerusalemu; anapaya batsogoleli bonse bantu na zofunka zawo zonse anazitumiza kuli mfumu ya ku Damasiko. \v 24 Ngakale kuti gulu yankondo inabwela na asilikali yochepa, Yehova anabapasa gulu yankondo ikulu kwambili, chifukwa Bayuda banasiya Yehova, Mulungu wa makolo wabo. Munjila iyi Ŵaaramu bana leta kuweluza kuli Yowashi.

1
24/25.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 25 Pa ntawi yamene Aaramu ana yenda, Yowasi anachitiwa vilonda maningi. Batumiki bake banamupangila chiwembu chifukwa cha magazi ya bana ba muna ba Yehoyada, wansembe. bana mupaila pa bedi pake, ndipo anafa; bana mushika mumanda mu Mzinda wa Davide, koma osati mumanda mwa mafumu. \v 26 Aba ni bantu bamene banamupangila chiwembu: Zabadi mwana mwamuna wa Simeati, mai wachi Amoni; na Yozabadi mwana mwamuna wa Simiriti, mkazi wa ku Moabu.

1
24/27.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 27 Manje nkani yokuza bana bake ba muna, uneneli wabwino wamene unakambiwa pali eve, na kumangamo nyumba ya Mulungu, onani, zinalembewa mu tendemanga ya buku ya mafumu. Amaziya + mwana wake mwamuna anayamba kulamulila mumalo mwake.

1
24/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 24

1
25/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 25 \v 1 Amaziya anali na zaka 25 pamene anayamba ku lamulila; analamulila na zaka 29 mu Yerusalemu. Amayi bake zina yabo inali Yehoadana, wa ku Yerusalemu. \v 2 Anachita zoyenera pamenso pa Yehova, koma osati na mtima onse.

1
25/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 China bwela monga mwamusanga kulamulila kwake kunali kosilizaka bwino, anapaya bantchito bamene banapaya batatebake, mfumu. \v 4 Koma sanafake bana babo ku infa, monga mwamene vinalembewa mubuku ya Mose, monga Yehova analamulila, "bazi tate babo sibafunika kupaiwa chifukwa cha bana babo, na bana sibafunikila kupaiwa chifukwa chazi tate babo. koma, muntu aliyense afunikila kufa chifukwa cha chimo yake."

1
25/05.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 5 Komanso, Amaziya anasonkanisa Bayuda pamozi, nakubelengesa monga ba munyumba ya makolo yabo, na asogoleli bambili, nabo lamulila mazana, ba Yuda bonse na Benjamini. Anababelega kuyambila zaka 20 kuyenda pasogolo, na kubapeza kuti banali bamuna osankiwa okwanila 300,000, okonzekela kuyena kunkondo. \v 6 Anangenesa bamuna bankondo bo chokela mu zana mu Israeli na matalente ya siliva.

1
25/07.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 7 Koma mwamuna wa Mulungu anabwela kuli eve nakukamba, "Mfumu, usavomeleze bankondo ba Israeli kuyenda naiwe, Yehova sali pakati pa Israeli- palibe muntu wa Efraimu. \v 8 Olo uyenda na kulimba mtima naku kosa kunkondo, Mulungu akuponya pansi pamenso pa mdani wako, pakuti Mulungu ndiye mphamvu yakutandiza, na mphamvu yakugwesa pansi.

1
25/09.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 9 Amaziya anakamba kuli muntu wa Mulungu kuti, "Koma tiza chita chani na matalente yamene yanapasiwa bankondo ba Israeli?" Muntu wa Mulungu anayanka, "Yehova akwanisa kukupasani zochuluka kuchila ivi." \v 10 Amaziya anapatula bankondo bamen banabwelae kuli eve kuchokela kuli Efraimu; anabaumiza kunyumba. Anakalipa maningi pa Yuda, na kubwelela kwabo na naukali oyaka moto.

1
25/11.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 11 Amaziya analimba mtima anasogolela bantu bake kuyenda kuchigwa cha Mchele; Kwamene kuja anagonjesa bamuna 10,000 baku Seiri. \v 12 Bankondo ba Yuda banatenga bamoyo bena 10,000. Anabatenga pamwamba pa tantwe na kubaponyela pansi kuchokela pamene paja, kuti bonse banapwanyika.

1
25/13.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 13 Koma bamuna bankondo bamene Amaziya anabweza, kuti basa yende na eve kunkondo, bana benya mu minzi ya Yuda kuyambila ku Samaliya kufikila ku Betihoroni. Anapaya bantu 3,000 na banatenga zofunka zambii.

2
25/14.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1,2 @@
\v 14 Manje chinabwela, Amaziya anabwelela kuchokela kokakanta Aedomu, analeta tu mulungu twa bantu ba ku Seiri, na kutuimika kunkala tu mulungu twake. Anatu
gwadila na kutushokela lubani. \v 15 Mwaicho ukali wa Yehova unayakila Amaziya. Anamtumizila mneneli wamene anakamba, "Chifukwa cha chani mwafuna tumilungu twa bantu bamene sanapulumuse bantu mumabja yabo?"

1
25/16.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 16 China bwela pamene mneneli anali kukamba naye, mfumu inakamba naye, "Takuika kuti unkale mlangizi wa mfumu? Leka! Nichifukwa cha chani uzapiliwa?" Mwaicho mneneli anya leka nakukamba, "Niziba kuti Mulungu aganiza zokuwonongani chifukwa mwachita ivi na simunamvele malangizo yanga."

1
25/17.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 17 Mwaicho Amaziya mfumu ya Yuda anafunsila upungu, anatumiza batumiki kuli Yoasi mwana wa Yoahazi mwana wa Yehu, mfumu ya Israeli, kuti, Tiyeni, tikumane wina na mnzake pankondo.

1
25/18.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 18 Koma Yoasi mfumu ya Israeli anatumiza amitenga kuli Amaziya mfumu ya Yuda, kuti, "Munga wa ku Lebano unatumiza utenga kuli mkunguza waku Lebano, kuti, Upase mwana wanga ankale mkazi, koma amtchile Chilombo cha ku Lebanoni chinausha na kupondaponda chisamba chaminga, \v 19 Wa kamba, 'Onani nakanta Edomu,' na mtima wako. Tenga kuzi nvela muku pambana kwako, koma unkale kunyumba, chifukwa ungazifake mukubvutika na kugwa iwe pamodzi na Yuda? ”

1
25/20.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 20 Koma Amaziya sanganvele, popeza ici chinacokela kuli Mulungu, kuti apeleke bantu ba Yuda mumanja mwa adani babo, popeza anafunsila kuli milungu ya Edomu. \v 21 Mwaicho Yoasi mfumu wa Israeli anatila nkondo; eve na Amaziya mfumu ya Yuda banakumana menso na mesno ku Beti Semesi, wa ku Yuda. \v 22 Bayuda banakantiwa pamenso pa Baisraeli, na aliyense anambululuka kwabo.

1
25/23.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 23 Yehoasi, mfumu wa Israeli, anagwila Amaziya mwana mwamuna wa Yehoasi mwana mwamuna wa Ahaziya, mfumu wa Yuda, pa Beti Shemesh. Bana muleta mu Yerusalemu na ku gwesa chipupa cha Yerusalemu kuchoka mu Ephraimu pongenela pa cona pongenela, mikono 400 mu utali. \v 24 Anatenga golide na siliva yonse, vonse vamene vinapezeka mu nyumba ya Mulungu na Obed-Edomu, na vintu va mtengo wapatali mu nyumba ya mfumu, na vogwiliwa, na kuwelela mu Samaria.

1
25/25.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 25 Amaziya mwana wa Yowasi mfumu ya Yuda anankala na moyo zaka kumi na zisanu pambuyo pa infa ya Yoasi mwana wa Yehoahazi mfumu ya Israeli. \v 26 Nkhani zina zokuza Amaziya, zoyambilila ai zomalizila, zinalembewa mubuku ya mafumu ya Yuda na Israeli.

1
25/27.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 27 Kuyambila pa ntawi yamene Amaziya anasiya kusatila Yehova, banayamba kumuchitila chiwembu ku Yerusalemu. Anambululuka ku Lakisi, koma banatumiza bamuna kumbuyo kwake ku Lakisi na kumupaya kwamene kuja. \v 28 Bana mubweza kukwela makavalo na kumuyika mumanda pamozi na makolo yake mu mzinda ya Yuda.

1
25/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 25

1
30/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 30 \v 1 Hezekiya anatumiza ntumi kuli Aisraeli bonse na Bayuda, ndipo analemba nkalata kuli Efraimu na Manase, kuti babwele ku nyumba ya Yehova ku Yerusalemu kubwela kuchita Paskha kuli Yehova, Mulungu wa Israeli. \v 2 Ndipo mfumu, nabasogoleli bake, na musonkano wonse wa mu Yerusalemu banakumana pamozi, nakusimikiza mitima kucita Paskha mumwezi wacibili. \v 3 sibanakwanise kuchita chikondwelelo pa ntau ya ntau zonse, chifukwa bansembe bang'ono benze banaziyelesa kuti bachite chikondwelelo chamene icho ndipi bantu benze bakalibe kukumana mu Yelusalemu.

1
30/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 Mau yamene aya yanaoneka bwino pamenso pa mfumu na mupingo onse. \v 5 mwa ichi anavomela kuti azibise Israeli yonse, kuyambila ku Beeriseba kufika ku Dani, kuti bantu babwele kuchita chikondwelelo cha Pasaka kuli Yehova, Mulungu wa Israeli, ku Yerusalemu. Pakuti benze bakalibe kuonapo ivi na gulu ikulu ya bantu, monga mwamene vinalembekela. \v 6 futi anatumiza na makalata yamene yanachoka kuli mfumu na basogoleli bake mu isilayeli yonse na yuda, kupitila mu lamulo ya mfumu. beve banakamba kuti, "imwe bantu ba Israeli, bwelelani kuli Yehova, Mulungu wa Abrahamu, Isaki ndi Israeli, kuti abwelele kuli bosala banu bamene banapulumuka mumanja mwa mafumu ba Asuri.

1
30/07.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 7 Musankale monga makolo yanu kapena babale banu, bamene banapondokela Yehova Mulungu wa makolo awo, nakubasandula chintu chonvesa manta, monga mwamene muonela. \v 8 manje musayumike mikosi yanu, mwamene yanachitila makolo yanu; koma, zipelekeni kuli Yehova ndipo mengene mumalo yake yoyela, bamene anapatula kwamuyayaya, mumulambile Yehova Mulungu wanu, kuti mukwiyo wake woyaka uchoke pali imwe. \v 9 Pakuti mukabwelela kuli Yehova, babale banu na bana banu bazachitiliwa chifundo pameso pa beve bamene anatengela kundende, ndipo bazabwelela kuziko ino. Chifukwa Yehova Mulungu wanu ni niwa bwino ndipo niwachifundo."

1
30/10.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 10 ndipo ntumi zija zinaenda kuchoka kumizinda namizinda ku mbali zonse za Efereimu na Manase, mpaka ku Zebuloni, koma bantu benze kungobaseka. \v 11 Koma, bamuna benango ba mutundu wa Aseri, Manase ndi Zebuloni banazichepesa na kubwela ku Yerusalemu. \v 12 Kwanja ya Mulungu inabwela futi pali Yuda, kubapasa mutima umozi, kuchita monga mwa lamulo ya mfumu na basogoleli mwa mau ya Yehova.

1
30/13.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 13 Bantu bambili bambili, gulu ikulu maningi, inakumana ku Yerusalemu kubwela kuchita chikondwelelo cha mikate ilibe chofufumisa mumwezi wachibili. \v 14 Beve bananyamuka nakuchosa maguwa yansembe yamene yanali mu Yerusalemu, na maguwa yansembe yonse ya vofukiza; banayaponya mumusinje wa Kidroni. \v 15 Ndipo banapaya bana ba nkosa ba pasika pa siku ya 14 ya mwezi wachibili. Bansembe na balevi banamvela nsoni, mwa ichi banaziyelesa na kubwelesa nsembe zopyeleza munyumba ya Yehova.

1
30/16.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 16 Bana imilila mumalo yao namagabanidwe yao, kukonka malangizo ya mulamulo ya Mose, muntu wa Mulungu. Bansembe bana mwaza magazi yamene banalandila kuchoka kuli ba levi. \v 17 Pakuti penze ba mbili mumusonkano bamene sibanaziyelese. Chifukwa chakayena Balevi banapaya bana ba nkosa ba Pasika kuli alionse osayeleseka, na bosakwanisa kupatula nsembe zao kuli Yehova.

1
30/18.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 18 Bantu bambili maningi, bambili bochokela ku Efereimu na Manase, Isakara ndi Zebuloni, sibenze banaziyelesa, koma banadya Pasika kukonka malangizo Pakuti Hezekiya enze anabapempelela kuti, "Yehova wabwino akululukile alionse \v 19 wamene ayika mutima wake pa kusakilasakila Mulungu, Yehova, Mulungu wa makolo yake, olo sanayelesewe na mayelesedwe ya mumalo yopatulika." \v 20 Ndipo Yehova anamvela Hezekiya, nakubapolesa bantu apo.

1
30/21.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 21 Bana ba Isiraeli bamene benze ku Yerusalemu banachita chikondwelelo cha mikate ilibe chofufumisa kwa masiku 7 mosangalala maningi. Balevi na bansembe ninshi batamanda Yehova siku na siku na voimbila vokwezeka Yehova. \v 22 Hezekiya anakamba molimbikisa Alevi bonse bamene benzo mvelela batumiki ba Yehova. beve banadya madyelelo masiku 7, na kupeleka nsembe zachiyanjano , na kuwululila Yehova Mulungu wa makolo yao.

1
30/23.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 23 Msonkano wonse uyu unaganiza kuyikako futi masiku yenango 7 yachikondwelelo. \v 24 Pakuti Hezekiya mfumu ya ku Yuda anapasa musonkano uyu wabantu ng'ombe zikazi chikwi chimozi na nkosa vikwi visanu na vibili; Basogoleli banapeleka ku mupingo ng'ombe zikazi 1,000, nkosa na mbuzi 10,000. Bansembe bambili banaziyelesa.

1
30/25.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 25 Gulu yonse ya Yuda, pamozi na bansembe na Balevi, na bantu bonse bamene banakumana kuchoka ku Israeli, koma futi balendo bochokela ku ziko ya Israeli na bonse bonkala mu Yuda — bonse banasangalala. \v 26 Manje kwenze chisangalalo chikulu mu Yerusalemu, pakuti kwenze kuyamba muntau ya Solomoni mwana wa Davide, mfumu ya Israeli, sikunankalepo vaso ku Yerusalemu. \v 27 Pamene apo bansembe, Balevi, banaimilila ndipo banadalisa bantu. Mau yao yanamveka, ndipo pempelo yao inakwela kumwamba, kumalo yoyela kwamene Mulungu ankala.

1
30/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 30

1
31/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 31 \v 1 Zonsezi zitatha, anthu onse a mu Israeli amene anali kumeneko anatuluka kupita ku mizinda ya ku Yuda nathyola zipilala zamiyala ndi kudula zipilala za Asera, naphwanya malo okwezeka ndi maguwa ansembe Yuda ndi Benjamini, ndi Efraimu ndi Manase, kufikira atawatha onse. Pamenepo anthu onse a Isiraeli anabwerera, aliyense kumalo ake ndi kumzinda wakwawo.

1
31/02.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 2 Hezekiya anagawa magulu a ansembe ndi Alevi m organizedmagulu awo, aliyense mogwirizana ndi ntchito yake, ansembe ndi Alevi. Anawaika kuti apereke nsembe zopsereza ndi nsembe zoyamika, kuti atumikire, kuthokoza, ndi kuyamika pazipata za nyumba ya Yehova. \v 3 Anaperekanso gawo la mfumu kuti likhale loperekera nsembe zopsereza kuchokera ku zinthu zake, kutanthauza nsembe zopsereza za m'mawa ndi madzulo, ndi nsembe zopsereza za pa Sabata, mwezi watsopano ndi nthawi ya chikondwerero, monga momwe zinalembedwera chilamulo cha Yehova.

1
31/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 Komanso, analamula anthu okhala mu Yerusalemu kuti apereke gawo la ansembe ndi Alevi, kuti apitilize kutsatira malamulo a Yehova. \v 5 Lamulolo litangotuluka, Aisraeli amapereka mowolowa manja zipatso zoyamba kucha za tirigu, vinyo watsopano, mafuta, uchi ndi zokolola zawo zonse za m fieldmunda. Anabweretsa chakhumi cha chilichonse, chomwe chinali chochuluka kwambiri.

1
31/06.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 6 Aisraeli ndi Ayuda omwe ankakhala m citiesmizinda ya Yuda ankabweretsanso chakhumi cha ng cattleombe ndi nkhosa, ndi chakhumi cha zinthu zopatulika zopatulidwira Yehova Mulungu wawo, ndipo anaziunjika milu milu. \v 7 Munali m'mwezi wachitatu pamene anayamba kuunjika mulu wa ndalama zawo, ndipo anamaliza mwezi wachisanu ndi chiwiri. \v 8 Hezekiya ndi atsogoleri atabwera ndi kuona miluyo, anatamanda Yehova ndi anthu ake Aisraeli.

1
31/09.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 9 Kenako Hezekiya anafunsa ansembe ndi Alevi za miluyo. \v 10 Azariya wansembe wamkulu wa mnyumba ya Zadoki anayankha kuti, “Kuyambira pamene anthu anayamba kubweretsa zopereka ku nyumba ya Yehova, tadya ndi kukhuta, ndipo tatsala ndi zotsala, pakuti Yehova wadalitsa anthu. Chomwe chatsala ndi kuchuluka kwakukulu uku kuno. "

1
31/11.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 11 Pamenepo Hezekiya analamula kuti zikonzedwe m'nyumba ya Yehova; ndipo anazikonzeratu. \v 12 Kenako anabweretsa mokhulupirika nsembe zopereka, chakhumi, ndi zinthu za Yehova. Kananiya Mlevi ndiye anali kuwayang'anira, ndipo m'bale wake Simeyi anali wachiwiri wake. \v 13 Yehieli, Azaziya, Nahati, Asaheli, Yerimoti, Yozabadi, Elieli, Isimakiya, Mahati, ndi Benaya anali oyang'anira pansi pa ulamuliro wa Konaniya ndi Simeyi m'bale wake, mwa kuikidwa ndi Hezekiya, mfumu, ndi Azariya, woyang'anira nyumba ya Mulungu .

1
31/14.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 14 Kore mwana wa Imna Mlevi, mlonda wa pachipata cha kummawa, anayang theanira zopereka zaufulu zoperekedwa ndi Mulungu, kuyang ofanira zopereka kwa Yehova ndi zopatulikitsa. \v 15 Pansi pake panali Edeni, Miniamini, Yesuwa, Semaya, Amariya, ndi Sekaniya, m'mizinda ya ansembe. Anadzaza maofesi odalilika, kuti apereke izi kwa abale awo magawano, onse ofunikira komanso osafunikira.

1
31/16.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 16 Anaperekanso kwa amuna onse a zaka zitatu kupita m'tsogolo, amene analembedwa m thebuku la makolo awo amene analowa m YahwehNyumba ya Yehova monga mwa dongosolo la tsiku ndi tsiku, kuti azigwira ntchito mu maudindo awo ndi misionszigawo zawo.

Some files were not shown because too many files have changed in this diff Show More