From c072133a1feafe6453811acfc3ea571d69c8ff41 Mon Sep 17 00:00:00 2001 From: Muzgatama Date: Thu, 18 Apr 2024 11:18:15 +0200 Subject: [PATCH] Thu Apr 18 2024 11:18:14 GMT+0200 (South Africa Standard Time) --- 11/18.txt | 2 +- 11/20.txt | 1 + 11/22.txt | 1 + 12/title.txt | 1 + manifest.json | 1 + 5 files changed, 5 insertions(+), 1 deletion(-) create mode 100644 11/20.txt create mode 100644 11/22.txt create mode 100644 12/title.txt diff --git a/11/18.txt b/11/18.txt index 1e35e00..014639b 100644 --- a/11/18.txt +++ b/11/18.txt @@ -1 +1 @@ -\v 18 \v 19 Rehobowamu anadzitengera mkazi: Mahalati, mwana wamkazi wa Yerimoti, mwana wa Davide, ndi Abihaili, mwana wamkazi wa Eliyabu, mwana wa Jese. Iye anamuberekera ana aamuna: Yeusi, Semariya ndi Zahamu. \ No newline at end of file +\v 18 Rehobowamu anadzitengera mkazi: Mahalati, mwana wamkazi wa Yerimoti, mwana wa Davide, ndi Abihaili, mwana wamkazi wa Eliyabu, mwana wa Jese. \v 19 Iye anamuberekera ana aamuna: Yeusi, Semariya ndi Zahamu. \ No newline at end of file diff --git a/11/20.txt b/11/20.txt new file mode 100644 index 0000000..820c6f8 --- /dev/null +++ b/11/20.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 20 Pambuyo pa Mahalati, Rehobowamu anatenga Maaka, mwana wamkazi wa Abisalomu; Iye anamuberekera Abiya, Atai, Ziza ndi Selomiti. \v 21 Rehobowamu anakonda Maaka mwana wamkazi wa Abisalomu koposa akazi ake onse ndi adzakazi ake onse (anatenga akazi khumi ndi asanu ndi atatu, ndi adzakazi makumi asanu ndi limodzi, nabala ana amuna makumi awiri mphambu asanu ndi atatu, ndi ana akazi makumi asanu ndi limodzi). \ No newline at end of file diff --git a/11/22.txt b/11/22.txt new file mode 100644 index 0000000..3c87f43 --- /dev/null +++ b/11/22.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 22 Rehobowamu anasankha Abiya mwana wa Maaka kukhala mtsogoleri, mtsogoleri pakati pa abale ake; anaganiza zomupanga kukhala mfumu. \v 23 Rehabiamu analamulira mwanzeru; Anabalalitsa ana ake onse aamuna mā€™dziko lonse la Yuda ndi Benjamini kumizinda yonse yamalinga. Anawapatsanso chakudya chochuluka ndipo ankawafunira akazi ambiri. \ No newline at end of file diff --git a/12/title.txt b/12/title.txt new file mode 100644 index 0000000..dfe3d1f --- /dev/null +++ b/12/title.txt @@ -0,0 +1 @@ +Mutu 12 \ No newline at end of file diff --git a/manifest.json b/manifest.json index d2a9386..1ba12b5 100644 --- a/manifest.json +++ b/manifest.json @@ -133,6 +133,7 @@ "11-11", "11-13", "11-16", + "11-18", "11-20", "11-22", "12-title",