Thu Apr 18 2024 11:30:17 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Timothy Muzgatama 2024-04-18 11:30:18 +02:00
parent 5507006a60
commit bd0ce5c297
4 changed files with 3 additions and 1 deletions

1
12/15.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 15 Nkhani zina zokhudza Rehobowamu, zoyamba ndi zomalizira, zinalembedwa mmabuku a mneneri Semaya ndi Ido wamasomphenya, mmabuku a mibadwo ya makolo awo ndi za nkhondo za nthawi zonse pakati pa Rehobowamu ndi Yerobiamu? \v 16 Nagona Rehabiamu ndi makolo ace, naikidwa m'mudzi wa Davide; Abiya mwana wake anakhala mfumu mmalo mwake.

1
13/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 13 \v 1 Mchaka cha 18 cha Mfumu Yerobiamu, Abiya anayamba kulamulira Yuda. \v 2 Anakhala mfumu zaka zitatu ku Yerusalemu; dzina la amake ndiye Makaya, mwana wamkazi wa Uriyeli wa ku Gibeya. Panali nkhondo pakati pa Abiya ndi Yerobiamu. \v 3 Abiya anapita kunkhondo ndi gulu lankhondo lamphamvu ndi olimba mtima, amuna osankhidwa 400,000. Yerobiamu anamuika ndi asilikali 800,000 osankhidwa mwapadera, ndi ngwazi zamphamvu.

1
13/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 13

View File

@ -146,7 +146,6 @@
"12-13",
"12-15",
"13-title",
"13-01",
"13-04",
"13-06",
"13-08",