From a6cf40cd394c97151f38b796192a409a6287650e Mon Sep 17 00:00:00 2001 From: Muzgatama Date: Thu, 18 Apr 2024 10:58:08 +0200 Subject: [PATCH] Thu Apr 18 2024 10:58:07 GMT+0200 (South Africa Standard Time) --- 10/06.txt | 2 +- 10/08.txt | 1 + 10/10.txt | 1 + manifest.json | 2 +- 4 files changed, 4 insertions(+), 2 deletions(-) create mode 100644 10/08.txt create mode 100644 10/10.txt diff --git a/10/06.txt b/10/06.txt index 5ddf9b5..a139ad3 100644 --- a/10/06.txt +++ b/10/06.txt @@ -1 +1 @@ -\v 6 \v 7 Mfumu Rehobiamu anafunsila uphungu ndi akulu amene anaimirira pamaso pa Solomo atate wake ali moyo; Adati: "Mundilangiza bwanji kuti ndiwayankhe anthu awa?" Iwo anamuuza kuti: “Mukawachitira zabwino anthuwa, ndi kuwasangalatsa, ndi kunena mawu abwino kwa iwo, adzakhala atumiki anu nthawi zonse. \ No newline at end of file +\v 6 Mfumu Rehobiamu anafunsila uphungu ndi akulu amene anaimirira pamaso pa Solomo atate wake ali moyo; Adati: "Mundilangiza bwanji kuti ndiwayankhe anthu awa?" \v 7 Iwo anamuuza kuti: “Mukawachitira zabwino anthuwa, ndi kuwasangalatsa, ndi kunena mawu abwino kwa iwo, adzakhala atumiki anu nthawi zonse. \ No newline at end of file diff --git a/10/08.txt b/10/08.txt new file mode 100644 index 0000000..381f66b --- /dev/null +++ b/10/08.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 8 Koma Rehobowamu ananyalanyaza uphungu wa akuluwo adamlangiza, nafunsira kwa anyamata anakulira naye, akuima pamaso pake. \v 9 Ndipo iye anati kwa iwo, Mundipangiranji uphungu, kuti tiyankhe anthu amene analankhula nane, kuti, Muchepetse goli limene atate wanu anatisenzetsa? \ No newline at end of file diff --git a/10/10.txt b/10/10.txt new file mode 100644 index 0000000..e6b9dd1 --- /dev/null +++ b/10/10.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 10 \v 11 Anyamata amene anakulira pamodzi ndi Rehobowamu anamuuza kuti: “Ukauze anthu amene anakuuzani kuti Solomo atate wanu analemetsa goli lawo, koma inu mulipeputse. ukawauze kuti, ‘Chala changa chaching’ono n’chachikulu kuposa chiuno cha atate wanga, ndipo tsopano, ngakhale kuti bambo anga anakusenzetsani goli lolemera, + ine ndidzakukwapulani ndi zikoti." \ No newline at end of file diff --git a/manifest.json b/manifest.json index 9c8a3c0..d0769d5 100644 --- a/manifest.json +++ b/manifest.json @@ -119,8 +119,8 @@ "10-title", "10-01", "10-03", + "10-06", "10-08", - "10-10", "10-12", "10-15", "10-16",