Thu Apr 18 2024 11:48:18 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Timothy Muzgatama 2024-04-18 11:48:19 +02:00
parent 7c11243acc
commit 996e9f632c
5 changed files with 5 additions and 2 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 7 Pakuti Asa anauza Yuda kuti: “Tiyeni timange mizinda iyi, timange mipanda yozungulira, ndi nsanja, zipata, mipiringidzo, dziko likadali lathu chifukwa tafunafuna Yehova Mulungu wathu. mbali zonse.” Choncho anamanga ndipo anapambana. \v 8 Asa anali ndi gulu lankhondo lonyamula zishango ndi mikondo; A fuko la Yuda anali ndi amuna 300,000, ndi a Benjamini amuna 280,000 onyamula zishango + ndi mauta. Onsewa anali ankhondo amphamvu.
\v 7 Pakuti Asa anauza Yuda kuti: “Tiyeni timange mizinda iyi, timange mipanda yozungulira, ndi nsanja, zipata, mipiringidzo, dziko likadali lathu chifukwa tafunafuna Yehova Mulungu wathu. mbali zonse.” Choncho anamanga ndipo anapambana. \v 8 Asa anali ndi gulu lankhondo lonyamula zishango ndi mikondo; A fuko la Yuda anali ndi amuna 300,000, ndi a Benjamini amuna 280,000 onyamula zishango ndi mauta. Onsewa anali ankhondo amphamvu.

1
14/09.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 9 Zera Mkusi anadza kwa iwo ndi khamu la asilikali miliyoni imodzi, ndi magareta mazana atatu; anafika ku Maresha. \v 10 Kenako Asa anatuluka kukakumana naye, ndipo anakonza mizere yankhondo mchigwa cha Zefata ku Maresha. \v 11 Asa anafuulira kwa Yehova Mulungu wake, nati, Yehova, palibe wina, koma Inu, wothandiza wopanda mphamvu polimbana ndi ambiri. tabwera kudzamenyana ndi unyinji uwu, Yehova, inu ndinu Mulungu wathu;

1
14/12.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 12 Momwemo Yehova anakantha Akusi pamaso pa Asa ndi Yuda; Akusi anathawa. \v 13 Asa ndi asilikali amene anali naye anawathamangitsa mpaka ku Gerari. Chotero akusi ambiri anaphedwa moti sanathenso kuchira, pakuti anawonongedwa kotheratu pamaso pa Yehova ndi gulu lake lankhondo. Gulu lankhondo linatenga zofunkha zambiri.

1
14/14.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
+ Koma khamu lankhondolo linawononga midzi yonse yozungulira Gerari, + pakuti kuopa + Yehova kunagwera okhalamo. Ankhondo anafunkha midzi yonse, ndipo munali zofunkha zambiri mmenemo. Ankhondowo anawononga mahema a oŵeta ngombe; + Anatenga nkhosa + zambirimbiri ndi ngamila, kenako anabwerera ku Yerusalemu.

View File

@ -158,9 +158,9 @@
"14-title",
"14-01",
"14-05",
"14-07",
"14-09",
"14-12",
"14-14",
"15-title",
"15-01",
"15-03",