From 8e497b425e55351020e78b4fbea1abf5b38720fe Mon Sep 17 00:00:00 2001 From: Muzgatama Date: Thu, 18 Apr 2024 12:04:22 +0200 Subject: [PATCH] Thu Apr 18 2024 12:04:21 GMT+0200 (South Africa Standard Time) --- 16/09.txt | 1 + 16/11.txt | 1 + 16/13.txt | 1 + 3 files changed, 3 insertions(+) create mode 100644 16/09.txt create mode 100644 16/11.txt create mode 100644 16/13.txt diff --git a/16/09.txt b/16/09.txt new file mode 100644 index 0000000..153b8ed --- /dev/null +++ b/16/09.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 9 Pakuti maso a Yehova ayang’ana pa dziko lonse lapansi, kuti adzionetsere wamphamvu kwa iwo amene mtima wawo uli wangwiro ndi Iye. Koma mwachita zopusa pankhaniyi. Kuyambira tsopano udzachita nkhondo.” \v 10 Pamenepo Asa anakwiyira wamasomphenyayo, ndipo anamuika m’ndende, pakuti anamukwiyira kwambiri pa nkhani imeneyi. \ No newline at end of file diff --git a/16/11.txt b/16/11.txt new file mode 100644 index 0000000..bca5a4d --- /dev/null +++ b/16/11.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 11 Taonani, machitidwe a Asa, kuyambira pachiyambi mpaka kumapeto, taonani, zalembedwa m'buku la mafumu a Yuda ndi Israeli. \v 12 M’chaka cha 39 cha ulamuliro wake, Asa anadwala matenda a mapazi ake. Ngakhale kuti matenda ake anali aakulu kwambiri, iye sanapemphe thandizo kwa Yehova, koma kwa ochiritsa okha. \ No newline at end of file diff --git a/16/13.txt b/16/13.txt new file mode 100644 index 0000000..86fd7bc --- /dev/null +++ b/16/13.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 13 Choncho Asa anagona pamodzi ndi makolo ake, ndipo anamwalira m’chaka cha 41 cha ufumu wake. \v 14 Iwo anamuika m’manda ake amene anadzikwirira mu Mzinda wa Davide. Anamugoneka pa chithatha chodzaza ndi fungo labwino ndi zonunkhira zosiyanasiyana zokonzedwa ndi odziwa kununkhira. Kenako anasonkha moto waukulu kwambiri pomulemekeza. \ No newline at end of file